الرئيسية تعرف على الإسلام CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO (Chichewa)
CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO

CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO (Chichewa)

قراءة الكتاب
عرض المحتوى باللغة العربية

CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO (Chichewa)

اللغة: Chichewa
إعداد: جمعية الدعوة بالروضة
نبذة مختصرة:
Cholinga cha bukhuli ndi kuwaunikira anthu omwe amafuna kudziwa zoona zokhazokha, pa zauthenga weniweni womwe Yesu (mtendere ukhale pa iye) ankaphunzitsa. Bukhuli likukamba za machitidwe ena omwe analetsedwa kapena kuvomerezedwa m’Baibulo. Pali chikhulupiliro chakuti anthu akawerenga bukhuli adzipezera okha gulu lenileni la anthu lomwe limatsatira chiphunzitso cha Yesu (mtendere ukhale pa iye). Umboni wochokera m’Baibulo ugwiritsidwa ntchito pofuna kuwaunikira awerengi athu chipembedzo chenicheni cha Yesu (mtendere ukhale pa iye) lero lino. Anthuwa ayenera kudziwa otsatira enieni a chiphunzitso cha Baibulo.